Genesis 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yokesani anabereka Sheba+ ndi Dedani.+ Ana a Dedani anali Asurimu, Letusimu ndi Leumimu. Yobu 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Magulu a amtengatenga a ku Tema+ amaifunafuna,Asabeya+ apaulendo amaidikirira.