Chivumbulutso 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndipo ataima patali poona kuzunzika kwake, adzati,+ ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe!+ Babulo iwe, mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi, chiweruzo chako chafika!’+
10 Ndipo ataima patali poona kuzunzika kwake, adzati,+ ‘Kalanga ine! Kalanga ine! Mzinda waukuluwe!+ Babulo iwe, mzinda wamphamvu! Chifukwa mu ola limodzi, chiweruzo chako chafika!’+