Miyambo 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Wodalira chuma chake adzagwa,+ koma anthu olungama adzasangalala ngati masamba a zomera.+ Miyambo 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+
11 Zinthu zamtengo wapatali za munthu wachuma ndizo mzinda wake wolimba,+ ndipo m’maganizo mwake zili ngati mpanda woteteza.+