Yesaya 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikwera pamwamba pamalo okwezeka a m’mitambo.+ Ndidzipanga kukhala wofanana ndi Wam’mwambamwamba.’+ Yeremiya 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu anzeru achita manyazi.+ Achita mantha ndipo adzagwidwa. Taonani! Iwo akana mawu a Yehova. Kodi ali ndi nzeru yotani tsopano?+
14 Ndikwera pamwamba pamalo okwezeka a m’mitambo.+ Ndidzipanga kukhala wofanana ndi Wam’mwambamwamba.’+
9 Anthu anzeru achita manyazi.+ Achita mantha ndipo adzagwidwa. Taonani! Iwo akana mawu a Yehova. Kodi ali ndi nzeru yotani tsopano?+