Malaki 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Anthu inu mudzapondaponda anthu oipa. Iwo adzakhala ngati fumbi kumapazi anu pa tsiku limene ndidzachitepo kanthu,”+ watero Yehova wa makamu.
3 “Anthu inu mudzapondaponda anthu oipa. Iwo adzakhala ngati fumbi kumapazi anu pa tsiku limene ndidzachitepo kanthu,”+ watero Yehova wa makamu.