-
Yesaya 62:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Taonani! Yehova wachititsa kuti mawu awa amveke mpaka kumadera akutali kwambiri a dziko lapansi:+ “Anthu inu, uzani mwana wamkazi wa Ziyoni+ kuti, ‘Taona! Chipulumutso chako chikubwera.+ Taona! Mphoto imene iye akufuna kupereka ili ndi iyeyo,+ ndipo malipiro amene akufuna kupereka ali pamaso pake.’”+
-