Yesaya 40:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Taonani! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzabwera ngati wamphamvu ndipo dzanja lake lizidzalamulira m’malo mwa iyeyo.+ Mphoto yake ili ndi iyeyo+ ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.+ Yesaya 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma ine ndinati: “Ndangovutika pachabe.+ Mphamvu zanga ndangoziwonongera zinthu zopanda pake ndi zachabechabe.+ Ndithu, Yehova ndiye amene adzandiweruze+ ndipo Mulungu wanga ndiye amene adzandipatse mphoto yanga.”+
10 Taonani! Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzabwera ngati wamphamvu ndipo dzanja lake lizidzalamulira m’malo mwa iyeyo.+ Mphoto yake ili ndi iyeyo+ ndipo malipiro amene amapereka ali pamaso pake.+
4 Koma ine ndinati: “Ndangovutika pachabe.+ Mphamvu zanga ndangoziwonongera zinthu zopanda pake ndi zachabechabe.+ Ndithu, Yehova ndiye amene adzandiweruze+ ndipo Mulungu wanga ndiye amene adzandipatse mphoto yanga.”+