Yeremiya 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 mafumu onse a Aluya,+ mafumu onse a anthu a mitundu yosiyanasiyana amene amakhala m’chipululu, Ezekieli 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amuna a ku Perisiya,+ ku Ludi+ ndi ku Puti+ anali m’gulu lako lankhondo, anali m’gulu la asilikali ako. Amuna amenewa anali kupachika zishango ndi zisoti mwa iwe.+ Iwo ndi amene anakuchititsa kukhala waulemerero.
10 Amuna a ku Perisiya,+ ku Ludi+ ndi ku Puti+ anali m’gulu lako lankhondo, anali m’gulu la asilikali ako. Amuna amenewa anali kupachika zishango ndi zisoti mwa iwe.+ Iwo ndi amene anakuchititsa kukhala waulemerero.