Yesaya 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzapereka Iguputo m’manja mwa mbuye wankhanza ndipo mfumu imene idzawalamulire idzakhala yamphamvu,”+ akutero Ambuye woona, Yehova wa makamu.
4 Ndidzapereka Iguputo m’manja mwa mbuye wankhanza ndipo mfumu imene idzawalamulire idzakhala yamphamvu,”+ akutero Ambuye woona, Yehova wa makamu.