Ezekieli 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inenso ndidzathyola nsonga ya pamwamba penipeni pa mtengo wa mkungudza.+ Ndidzabudula nsonga yanthete kunthambi zake+ ndipo ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali.+
22 “‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inenso ndidzathyola nsonga ya pamwamba penipeni pa mtengo wa mkungudza.+ Ndidzabudula nsonga yanthete kunthambi zake+ ndipo ndidzaibzala pamwamba pa phiri lalitali.+