Danieli 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mlondayo anali kulankhula mofuula kuti: “Gwetsani mtengowo+ ndipo dulani nthambi zake. Yoyolani masamba ake ndi kumwaza zipatso zake. Nyama zithawe pansi pake ndipo mbalame zichoke panthambi zake,+
14 Mlondayo anali kulankhula mofuula kuti: “Gwetsani mtengowo+ ndipo dulani nthambi zake. Yoyolani masamba ake ndi kumwaza zipatso zake. Nyama zithawe pansi pake ndipo mbalame zichoke panthambi zake,+