Genesis 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Semu anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi ndi Aramu. Yeremiya 49:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yehova anauza Yeremiya mawu okhudza Elamu+ kuchiyambi kwa ufumu wa Zedekiya+ mfumu ya Yuda, kuti: