Genesis 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Semu anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi ndi Aramu. Yesaya 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pali masomphenya ochititsa mantha+ amene ndaona: Mtundu wochita chinyengo ukuchita zachinyengo, ndipo mtundu wolanda zinthu ukulanda zinthu.+ Pita ukachite nkhondo, iwe Elamu! Kazungulire mzindawo, iwe Mediya!+ Ndathetsa kuusa moyo* konse kumene mzindawo unachititsa.+ Yeremiya 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 mafumu onse a Zimiri, mafumu onse a Elamu,+ mafumu onse a Amedi,+ Ezekieli 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Kumandako n’kumene kuli Elamu+ ndi khamu lake lonse. Khamu lakelo linaikidwa mozungulira manda ake. Onsewo anaphedwa ndi lupanga. Iwo anatsikira kunthaka ali osadulidwa. Amenewa anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo, ndipo adzanyozeka limodzi ndi onse otsikira kudzenje.+ Danieli 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nditayamba kuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani,+ imene ili m’chigawo cha Elamu.+ M’masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili m’mphepete mwa mtsinje wa Ulai.+ Machitidwe 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakati pathu pali Apati, Amedi,+ ndi Aelamu.+ Palinso anthu ochokera ku Mesopotamiya, ku Yudeya,+ ku Kapadokiya,+ ku Ponto+ ndi kuchigawo cha Asia.+
2 Pali masomphenya ochititsa mantha+ amene ndaona: Mtundu wochita chinyengo ukuchita zachinyengo, ndipo mtundu wolanda zinthu ukulanda zinthu.+ Pita ukachite nkhondo, iwe Elamu! Kazungulire mzindawo, iwe Mediya!+ Ndathetsa kuusa moyo* konse kumene mzindawo unachititsa.+
24 “‘Kumandako n’kumene kuli Elamu+ ndi khamu lake lonse. Khamu lakelo linaikidwa mozungulira manda ake. Onsewo anaphedwa ndi lupanga. Iwo anatsikira kunthaka ali osadulidwa. Amenewa anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo, ndipo adzanyozeka limodzi ndi onse otsikira kudzenje.+
2 Nditayamba kuona masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili kunyumba ya mfumu yokhala ndi mpanda wolimba kwambiri ya ku Susani,+ imene ili m’chigawo cha Elamu.+ M’masomphenyawo ndinapezeka kuti ndili m’mphepete mwa mtsinje wa Ulai.+
9 Pakati pathu pali Apati, Amedi,+ ndi Aelamu.+ Palinso anthu ochokera ku Mesopotamiya, ku Yudeya,+ ku Kapadokiya,+ ku Ponto+ ndi kuchigawo cha Asia.+