Mateyu 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 amene ali mu Yudeya adzayambe kuthawira+ kumapiri. Maliko 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho onse okhala m’dera la Yudeya ndi onse okhala mu Yerusalemu anakhamukira kwa iye. Chotero iye anawabatiza mumtsinje wa Yorodano ndipo anthuwo anali kuulula machimo awo poyera.+
5 Choncho onse okhala m’dera la Yudeya ndi onse okhala mu Yerusalemu anakhamukira kwa iye. Chotero iye anawabatiza mumtsinje wa Yorodano ndipo anthuwo anali kuulula machimo awo poyera.+