-
Ezekieli 32:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Elamu+ ali kumandako limodzi ndi gulu la anthu ake onse amene ankamutsatira ndipo anthuwo azungulira manda ake. Onsewo anaphedwa ndi lupanga. Iwo anatsikira kunthaka ali osadulidwa. Anthu amenewa anachititsa kuti anthu amene akukhala mʼdziko la anthu amoyo azikhala mwamantha. Tsopano anthu amenewa adzachita manyazi limodzi ndi anthu amene akutsikira kudzenje.*
-