1 Samueli 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 N’chifukwa chiyani anthu inu mukunyozabe nsembe zanga+ zimene ndinalamula m’nyumba yanga,+ n’kumalemekezabe ana anu koposa ine mwa kudzinenepetsa+ ndi mbali yabwino kwambiri ya nsembe iliyonse ya anthu anga Aisiraeli?+
29 N’chifukwa chiyani anthu inu mukunyozabe nsembe zanga+ zimene ndinalamula m’nyumba yanga,+ n’kumalemekezabe ana anu koposa ine mwa kudzinenepetsa+ ndi mbali yabwino kwambiri ya nsembe iliyonse ya anthu anga Aisiraeli?+