1 Samueli 17:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo ine ndinatsatira chilombocho n’kuchipha,+ ndipo ndinapulumutsa nkhosa m’kamwa mwake. Chitayamba kundiukira, ndinagwira ndevu zake, n’kuchikantha ndi kuchipha.
35 Pamenepo ine ndinatsatira chilombocho n’kuchipha,+ ndipo ndinapulumutsa nkhosa m’kamwa mwake. Chitayamba kundiukira, ndinagwira ndevu zake, n’kuchikantha ndi kuchipha.