Ezekieli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa zamoyo zinayizo, chamoyo chilichonse chinali ndi nkhope zinayi+ ndi mapiko anayi, ndipo kupansi kwa mapiko awo kunali zinthu zooneka ngati manja a munthu.
21 Pa zamoyo zinayizo, chamoyo chilichonse chinali ndi nkhope zinayi+ ndi mapiko anayi, ndipo kupansi kwa mapiko awo kunali zinthu zooneka ngati manja a munthu.