Yeremiya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+
16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+