Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Usagwiritse ntchito dzina la Yehova Mulungu wako mosasamala,+ pakuti Yehova sadzalekerera aliyense wogwiritsa ntchito dzina lake mosasamala osam’langa.+

  • Salimo 74:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kumbukirani izi: Inu Yehova, mdani wakuchitirani mopanda ulemu,+

      Ndipo anthu opusa anyoza dzina lanu.+

  • Yesaya 48:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndidzabweza mkwiyo wanga chifukwa cha dzina langa,+ ndipo chifukwa cha ulemerero wanga, ine ndidzadziletsa kuti ndisakuwonongeni.+

  • Yesaya 52:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Tsopano kodi pamenepa ndichitepo chiyani?” akutero Yehova. “Pakuti anthu anga anatengedwa popanda malipiro alionse.+ Amene anali kuwalamulira ankangokhalira kufuula.+ Nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu, dzina langa anali kulichitira chipongwe,”+ akutero Yehova.

  • Ezekieli 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma ine ndinachita zinthu molemekeza dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina amene iwo anali kukhala pakati pawo,+ pakuti ndinawachititsa kuti andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo powatulutsa m’dziko la Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena