Yesaya 66:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mudzaona zimenezi ndipo mtima wanu udzasangalala.+ Mafupa anu+ adzakhala ndi mphamvu ngati udzu wobiriwira.+ Dzanja la Yehova lidzadziwika kwa atumiki ake,+ koma iye adzakwiyira adani ake.”+ Chivumbulutso 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masiku atatu ndi hafu+ aja atatha, mzimu wa moyo wochokera kwa Mulungu unalowa mwa mboni zija.+ Ndiyeno mbonizo zinaimirira, ndipo amene anali kuziona anagwidwa ndi mantha aakulu.
14 Mudzaona zimenezi ndipo mtima wanu udzasangalala.+ Mafupa anu+ adzakhala ndi mphamvu ngati udzu wobiriwira.+ Dzanja la Yehova lidzadziwika kwa atumiki ake,+ koma iye adzakwiyira adani ake.”+
11 Masiku atatu ndi hafu+ aja atatha, mzimu wa moyo wochokera kwa Mulungu unalowa mwa mboni zija.+ Ndiyeno mbonizo zinaimirira, ndipo amene anali kuziona anagwidwa ndi mantha aakulu.