Miyambo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zimenezi zidzachiritsa+ mchombo wako ndi kutsitsimutsa mafupa ako.+ Miyambo 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mtima wosangalala ndiwo mankhwala ochiritsa,+ koma mtima wosweka umaumitsa mafupa.+