Numeri 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+ Ezekieli 36:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthu a mitundu ina okuzungulirani amene adzatsale, adzadziwa kuti ine Yehova, ndamanga zinthu zimene zinagwetsedwa.+ Adzadziwa kuti ndabzala mitengo m’dziko limene linali bwinja. Ine Yehova ndanena zimenezi ndipo ndazichita.’+
19 Mulungu si munthu, woti anganene mabodza,+Si mwana wa munthu, woti angadzimve kuti ali ndi mlandu.+Kodi ananenapo kanthu koma osachita,Analankhulapo kanthu kodi koma osakwaniritsa?+
36 Anthu a mitundu ina okuzungulirani amene adzatsale, adzadziwa kuti ine Yehova, ndamanga zinthu zimene zinagwetsedwa.+ Adzadziwa kuti ndabzala mitengo m’dziko limene linali bwinja. Ine Yehova ndanena zimenezi ndipo ndazichita.’+