Ezekieli 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Itiyopiya,+ Puti,+ Ludi, anthu onse ochokera ku mitundu ina,+ Kubi ndi anthu ochokera m’dziko la Isiraeli amene ali m’pangano, onsewa adzaphedwa ndi lupanga pamodzi ndi Aiguputo.”’+
5 Itiyopiya,+ Puti,+ Ludi, anthu onse ochokera ku mitundu ina,+ Kubi ndi anthu ochokera m’dziko la Isiraeli amene ali m’pangano, onsewa adzaphedwa ndi lupanga pamodzi ndi Aiguputo.”’+