Ezekieli 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Dedani+ unali kuchita nawo malonda, ndipo unalemba ntchito zilumba zambiri kuti zizikuchitira malonda. Anthu a m’zilumbazo anali kukulipira minyanga+ komanso mitengo ya phingo.
15 Ana a Dedani+ unali kuchita nawo malonda, ndipo unalemba ntchito zilumba zambiri kuti zizikuchitira malonda. Anthu a m’zilumbazo anali kukulipira minyanga+ komanso mitengo ya phingo.