Ezekieli 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako ananditengera kutsogolo kwa Nyumba ija kudzera pachipata cha kumpoto kuti ndikaone zimene zinali kumeneko. Kumeneko ndinaona ulemerero wa Yehova utadzaza m’nyumba ya Yehova.+ Pamenepo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+
4 Kenako ananditengera kutsogolo kwa Nyumba ija kudzera pachipata cha kumpoto kuti ndikaone zimene zinali kumeneko. Kumeneko ndinaona ulemerero wa Yehova utadzaza m’nyumba ya Yehova.+ Pamenepo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi.+