1 Mafumu 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+ Ezekieli 43:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Ansembe achilevi+ omwe ndi ana a Zadoki,+ amene amayandikira kwa ine ndi kunditumikira,+ uwapatse ng’ombe yaing’ono yamphongo kuchokera pagulu la ziweto kuti ikhale nsembe yamachimo.’+ Watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+
19 “‘Ansembe achilevi+ omwe ndi ana a Zadoki,+ amene amayandikira kwa ine ndi kunditumikira,+ uwapatse ng’ombe yaing’ono yamphongo kuchokera pagulu la ziweto kuti ikhale nsembe yamachimo.’+ Watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.