-
Ezekieli 42:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Zipinda zodyeramo zam’mwamba zinali zocheperapo chifukwa chakuti makondewo anatengako malo ena a zipindazo. Zipinda zimenezi zinali zocheperapo kusiyana ndi zapakati komanso zapansi.
-