Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 6:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Zitseko ziwirizo zinali za matabwa a mtengo wa mafuta. Pazitsekopo anajambulapo mochita kugoba akerubi, mitengo ya kanjedza, ndi maluwa, ndipo anazikuta ndi golide. Kenako akerubi ndi mitengo ya kanjedza yolemba mochita kugoba ya pazitsekozo, anazikuta ndi golide.

  • 2 Mbiri 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 zozimitsira nyale, mbale zolowa, makapu, ndi zopalira moto. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Anapanganso khomo lolowera m’nyumbayo,+ zitseko zamkati za Chipinda Choyera Koposa, ndi zitseko+ za nyumbayo. Zonsezi zinali zagolide.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena