Ekisodo 29:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho uzipereka ng’ombe ya nsembe yamachimo tsiku ndi tsiku kuti iphimbe machimo.+ Pamenepo uziyeretsa guwa lansembe ku machimo mwa kuliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza+ kuti likhale loyera. Levitiko 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mafuta onse a mbuziyo aziwatentha paguwa lansembe mofanana ndi mafuta a nsembe yachiyanjano.+ Pamenepo wansembe aziphimba tchimo la mtsogoleriyo,+ ndipo azikhululukidwa.
36 Choncho uzipereka ng’ombe ya nsembe yamachimo tsiku ndi tsiku kuti iphimbe machimo.+ Pamenepo uziyeretsa guwa lansembe ku machimo mwa kuliperekera nsembe yophimba machimo, ndipo uzilidzoza+ kuti likhale loyera.
26 Mafuta onse a mbuziyo aziwatentha paguwa lansembe mofanana ndi mafuta a nsembe yachiyanjano.+ Pamenepo wansembe aziphimba tchimo la mtsogoleriyo,+ ndipo azikhululukidwa.