Ekisodo 28:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndipo uwapangire makabudula ansalu ofika m’ntchafu kuti azibisa maliseche awo.+