-
Ezekieli 48:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 “Malo onse oti aperekedwewo akhale aatali mikono 25,000 mbali iyi ndi mikono 25,000 mbali inayo. Anthu inu mupereke malo ofanana mbali zonse kuti akhale chopereka chopatulika ndiponso malo a mzinda.
-