Ezekieli 48:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Gawo limeneli likhale la ansembe opatulika, ana a Zadoki,+ amene amanditumikira. Iwo sanandisiye ngati mmene anandisiyira Alevi amene anatsata ana a Isiraeli.+
11 Gawo limeneli likhale la ansembe opatulika, ana a Zadoki,+ amene amanditumikira. Iwo sanandisiye ngati mmene anandisiyira Alevi amene anatsata ana a Isiraeli.+