-
Ezekieli 46:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Mtsogoleri wa anthu akapereka mphatso kwa mwana wake aliyense wamwamuna monga cholowa chake, mphatsoyo idzakhala chuma cha mwanayo. Chimenecho ndi chuma cha anawo ndipo chidzakhala cholowa chawo.
-