Yesaya 66:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova.
23 “Kuyambira mwezi watsopano mpaka mwezi wina watsopano, ndiponso sabata ndi sabata, anthu onse adzabwera kudzagwada pamaso panga,”+ watero Yehova.