2 Mbiri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Atangomaliza kupereka nsembeyo, mfumu ndi onse amene anali nayo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+
29 Atangomaliza kupereka nsembeyo, mfumu ndi onse amene anali nayo anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi.+