1 Mbiri 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu. 2 Mbiri 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi yomweyo Yehosafati anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo Ayuda onse ndi anthu okhala mu Yerusalemu anawerama pamaso pa Yehova kuti alambire Yehovayo.+ Salimo 72:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mafumu onse adzamugwadira ndi kumuweramira.+Ndipo mitundu yonse ya anthu idzamutumikira.+
20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu.
18 Nthawi yomweyo Yehosafati anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi,+ ndipo Ayuda onse ndi anthu okhala mu Yerusalemu anawerama pamaso pa Yehova kuti alambire Yehovayo.+