Levitiko 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Zikondwerero+ za Yehova zimene muyenera kulengeza+ ndiyo misonkhano yopatulika. Izi ndi zikondwerero zanga: Numeri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Lizikhala tsiku lanu loliza lipenga.+ Deuteronomo 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+
2 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Zikondwerero+ za Yehova zimene muyenera kulengeza+ ndiyo misonkhano yopatulika. Izi ndi zikondwerero zanga:
29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Lizikhala tsiku lanu loliza lipenga.+
10 Ndiyeno uzichitira Yehova Mulungu wako+ chikondwerero cha masabata, popereka nsembe zaufulu zimene ungathe, monga mmene Yehova Mulungu wako angakudalitsire.+