Ezekieli 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mawilowo akamayenda, anali kulowera kumbali zonse zinayi+ ndipo sanali kukhotera kwina.+