-
Ezekieli 1:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kulikonse kumene mzimu ukufuna kupita, zamoyozo zinali kupita kumeneko, chifukwa mzimuwo wafuna kuti upite kumeneko. Mawilowo anali kukwera m’mwamba ali pambali pa zamoyozo, pakuti mzimu wa zamoyozo unali m’mawilowo.
-