-
Yeremiya 1:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Yehova anandifunsanso kachiwiri kuti: “Ukuona chiyani?”
Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mphika wakukamwa kwakukulu umene uli pamoto, ndipo motowo aupemerera kuti uyake kwambiri. Mphikawo wafulatira kumpoto.”
-