Yeremiya 29:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Anthu onse amene ali ku ukapolo uwatumizire uthenga+ wakuti, ‘Ponena za Semaya wa ku Nehelamu, Yehova wanena kuti: “Pakuti Semaya walosera kwa anthu inu, ngakhale kuti ine sindinamutume, ndipo wayesa kukuchititsani kukhulupirira zinthu zonama,+
31 “Anthu onse amene ali ku ukapolo uwatumizire uthenga+ wakuti, ‘Ponena za Semaya wa ku Nehelamu, Yehova wanena kuti: “Pakuti Semaya walosera kwa anthu inu, ngakhale kuti ine sindinamutume, ndipo wayesa kukuchititsani kukhulupirira zinthu zonama,+