Ekisodo 24:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ulemerero wa Yehova+ unakhalabe paphiri la Sinai,+ ndipo mtambowo unakutabe phirilo kwa masiku 6. Ndiyeno pa tsiku la 7, Mulungu anaitana Mose kuchokera mumtambowo.+ Ezekieli 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kumeneko ndinaonako ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli,+ wofanana ndi zimene ndinaona kuchigwa zija.
16 Ulemerero wa Yehova+ unakhalabe paphiri la Sinai,+ ndipo mtambowo unakutabe phirilo kwa masiku 6. Ndiyeno pa tsiku la 7, Mulungu anaitana Mose kuchokera mumtambowo.+