Ezekieli 23:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Kudzabwera khamu la anthu kudzawaukira+ ndi kuwasandutsa chinthu chochititsa mantha komanso chinthu choyenera kutengedwa ndi adani.+ Habakuku 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+
46 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Kudzabwera khamu la anthu kudzawaukira+ ndi kuwasandutsa chinthu chochititsa mantha komanso chinthu choyenera kutengedwa ndi adani.+
6 Ine ndikuutsa Akasidi,+ mtundu waukali ndi waphuma umene ukupita kumalo otakasuka a padziko lapansi kukatenga malo amene si awo.+