Ezekieli 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndithu, ine ndidzathetsa khalidwe lotayirira mwa iwe+ ndiponso uhule wako umene unachoka nawo kudziko la Iguputo.+ Sudzakwezanso maso ako kuyang’ana amuna a ku Iguputo ndipo dziko la Iguputo sudzalikumbukiranso.’
27 Ndithu, ine ndidzathetsa khalidwe lotayirira mwa iwe+ ndiponso uhule wako umene unachoka nawo kudziko la Iguputo.+ Sudzakwezanso maso ako kuyang’ana amuna a ku Iguputo ndipo dziko la Iguputo sudzalikumbukiranso.’