Ezara 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+ Ezekieli 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino.+ Mudzanyansidwa ndi zochita zanu, zolakwa zanu ndi zinthu zonyansa zimene munachita.+
6 Kenako ndinayamba kunena kuti:+ “Inu Mulungu wanga, ndikuchita manyazi+ kuti ndikweze nkhope yanga kwa inuyo Mulungu wanga, chifukwa zolakwa zathu+ zachuluka pamutu pathu ndipo machimo athu achuluka kwambiri mpaka kufika kumwamba.+
31 Choncho mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino.+ Mudzanyansidwa ndi zochita zanu, zolakwa zanu ndi zinthu zonyansa zimene munachita.+