Yesaya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mukakhala ndi mtima wofuna kundimvera, mudzadya zabwino za m’dziko lanu.+ Ezekieli 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+ Aefeso 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.
19 Ndidzawapatsa mtima umodzi+ ndipo ndidzaika mzimu watsopano mwa iwo.+ Ndidzachotsa mtima wamwala m’matupi awo+ n’kuwapatsa mtima wamnofu,+
24 ndi kuvala+ umunthu watsopano+ umene unalengedwa+ mogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu ndipo umatsatira zofunika pa chilungamo chenicheni+ ndi pa kukhulupirika.