Ezekieli 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano akuluakulu a Isiraeli anabwera kwa ine n’kudzakhala pamaso panga.+