Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 M’chaka cha 6, m’mwezi wa 6, pa tsiku lachisanu la mweziwo, ndinali nditakhala m’nyumba mwanga ndipo akuluakulu a Yuda anali atakhala pamaso panga.+ Pamenepo, dzanja la Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, linafika pa ine.+

  • Ezekieli 20:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 M’chaka cha 7, m’mwezi wachisanu, pa tsiku la 10 la mweziwo, akuluakulu a Isiraeli anabwera kwa ine kudzafunsira kwa Yehova,+ ndipo anakhala pamaso panga.+

  • Ezekieli 33:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Iwo adzabwera kwa iwe ngati mmene amachitira nthawi zonse ndipo adzakhala pamaso pako ngati anthu anga.+ Adzamva mawu ako koma sadzawatsatira,+ chifukwa ndi pakamwa pawo, akulankhula za zilakolako zawo zonyansa ndipo mtima wawo uli pa kupeza phindu mopanda chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena