Ezekieli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’chaka cha 6, m’mwezi wa 6, pa tsiku lachisanu la mweziwo, ndinali nditakhala m’nyumba mwanga ndipo akuluakulu a Yuda anali atakhala pamaso panga.+ Pamenepo, dzanja la Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, linafika pa ine.+
8 M’chaka cha 6, m’mwezi wa 6, pa tsiku lachisanu la mweziwo, ndinali nditakhala m’nyumba mwanga ndipo akuluakulu a Yuda anali atakhala pamaso panga.+ Pamenepo, dzanja la Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, linafika pa ine.+